Koma panali munthu wa Afarisi, dzina lake Nikodemo, mkulu wa Ayuda. ⓠIyeyu anadza kwa Yesu usiku, nati kwa Iye, Rabi, tidziwa kuti Inu ndinu mphunzitsi wochokera kwa Mulungu; pakuti palibe munthu akhoza kuchita zizindikiro zimene Inu muchita, ngati Mulungu sakhala naye. …
← Back to Chichewa Bible
Loading…